Deuteronomo 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndileke ndiwawononge+ ndi kufafaniza dzina lawo pansi pa thambo,+ ndipo ndikupange mtundu wamphamvu ndi waukulu kwambiri kuposa iwo.’+ Aroma 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikanakonda kuti ineyo ndichotsedwe kwa Khristu monga wotembereredwa m’malo mwa abale anga,+ amene ali anthu a mtundu wanga.+
14 Ndileke ndiwawononge+ ndi kufafaniza dzina lawo pansi pa thambo,+ ndipo ndikupange mtundu wamphamvu ndi waukulu kwambiri kuposa iwo.’+
3 Ndikanakonda kuti ineyo ndichotsedwe kwa Khristu monga wotembereredwa m’malo mwa abale anga,+ amene ali anthu a mtundu wanga.+