Aroma 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Moni kwa Anduroniko ndi Yuniya, omwe ndi achibale anga+ ndi akaidi anzanga.+ Amenewa ndi amuna odziwika kwambiri kwa atumwi ndiponso akhala ogwirizana+ ndi Khristu kwa nthawi yaitali kuposa ine. Aroma 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Wantchito mnzanga Timoteyo akupereka moni, chimodzimodzinso Lukiyo, Yasoni ndi Sosipato omwe ndi achibale anga.+
7 Moni kwa Anduroniko ndi Yuniya, omwe ndi achibale anga+ ndi akaidi anzanga.+ Amenewa ndi amuna odziwika kwambiri kwa atumwi ndiponso akhala ogwirizana+ ndi Khristu kwa nthawi yaitali kuposa ine.
21 Wantchito mnzanga Timoteyo akupereka moni, chimodzimodzinso Lukiyo, Yasoni ndi Sosipato omwe ndi achibale anga.+