Aroma 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikanakonda kuti ineyo ndichotsedwe kwa Khristu monga wotembereredwa m’malo mwa abale anga,+ amene ali anthu a mtundu wanga.+ Aroma 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Moni kwa wachibale wanga+ Herodiona. Moni kwa a m’banja la Narikiso amene ali mwa Ambuye.+
3 Ndikanakonda kuti ineyo ndichotsedwe kwa Khristu monga wotembereredwa m’malo mwa abale anga,+ amene ali anthu a mtundu wanga.+