Yohane 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 kuti onsewa akhale amodzi,+ mmene inu Atate ndi ine tilili ogwirizana,+ kuti iwonso akhale ogwirizana ndi ife,+ ndi kuti dziko likhulupirire kuti inu munanditumadi.+ Afilipi 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo ndili pamodzi ndi Timoteyo monga akapolo+ a Khristu Yesu. Ndikulembera oyera onse ogwirizana ndi Khristu Yesu amene ali ku Filipi,+ komanso oyang’anira ndi atumiki othandiza:+
21 kuti onsewa akhale amodzi,+ mmene inu Atate ndi ine tilili ogwirizana,+ kuti iwonso akhale ogwirizana ndi ife,+ ndi kuti dziko likhulupirire kuti inu munanditumadi.+
1 Ine Paulo ndili pamodzi ndi Timoteyo monga akapolo+ a Khristu Yesu. Ndikulembera oyera onse ogwirizana ndi Khristu Yesu amene ali ku Filipi,+ komanso oyang’anira ndi atumiki othandiza:+