Machitidwe 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Titachoka kumeneko tinafika ku Filipi,+ mzinda umene uli pansi pa ulamuliro wa Roma, umenenso ndi likulu la chigawo cha Makedoniya.+ Tinakhala mumzinda umenewu kwa masiku ndithu.
12 Titachoka kumeneko tinafika ku Filipi,+ mzinda umene uli pansi pa ulamuliro wa Roma, umenenso ndi likulu la chigawo cha Makedoniya.+ Tinakhala mumzinda umenewu kwa masiku ndithu.