Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 11:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 M’tsiku limenelo, Yehova adzaperekanso dzanja lake kachiwiri+ kuti atenge anthu ake otsala kuchokera ku Asuri,+ ku Iguputo,+ ku Patirosi,+ ku Kusi,+ ku Elamu,+ ku Sinara,+ ku Hamati ndi m’zilumba za m’nyanja.+

  • Yeremiya 31:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova wanena kuti: “Fuulirani Yakobo mosangalala, fuulani kwambiri muli patsogolo pa mitundu ina ya anthu.+ Lengezani zimenezi.+ Tamandani Mulungu ndi kunena kuti, ‘Inu Yehova, pulumutsani anthu anu, otsalira a Isiraeli.’+

  • Mika 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anthu amene anali kuyenda motsimphina ndidzawasonkhanitsanso pamodzi monga anthu otsala.+ Anthu amene anawachotsa m’dziko lawo ndi kuwapititsa kutali ndidzawasandutsa mtundu wamphamvu.+ Yehova adzawalamulira monga mfumu m’phiri la Ziyoni kuyambira nthawi imeneyo mpaka kalekale.+

  • Aroma 9:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Komanso, Yesaya analankhula mofuula zokhudza Isiraeli kuti: “Ngakhale kuti ana a Isiraeli adzakhala ochuluka ngati mchenga wa m’nyanja,+ ndi ochepa okha amene adzapulumuke.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena