Zekariya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anandiyankha kuti: “Akupita nacho kudziko la Sinara+ kuti akamangire+ mkaziyo nyumba kumeneko. Akamumangira nyumba yolimba ndipo akamukhazika kumeneko pamalo ake oyenera.”
11 Iye anandiyankha kuti: “Akupita nacho kudziko la Sinara+ kuti akamangire+ mkaziyo nyumba kumeneko. Akamumangira nyumba yolimba ndipo akamukhazika kumeneko pamalo ake oyenera.”