Zekariya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anandiyankha kuti: “Akupita nacho kudziko la Sinara*+ kuti akamangire mzimayiyo nyumba kumeneko. Akakamumangira nyumbayo, akamukhazika kumeneko pamalo ake oyenera.” Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:11 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, ptsa. 24-25
11 Iye anandiyankha kuti: “Akupita nacho kudziko la Sinara*+ kuti akamangire mzimayiyo nyumba kumeneko. Akakamumangira nyumbayo, akamukhazika kumeneko pamalo ake oyenera.”