Yesaya 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti iwe Isiraeli, ngakhale anthu ako atakhala ngati mchenga wa kunyanja,+ otsala ochepa okha pakati pawo ndi amene adzabwerere.+ Chiwonongeko+ chimene Mulungu wakonzera anthu awa chidzabwera mwachilungamo ngati madzi osefukira,+ Aroma 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero, pa nthawi ino alipo ena ochepa+ amene anasankhidwa+ mwa kukoma mtima kwakukulu.
22 Pakuti iwe Isiraeli, ngakhale anthu ako atakhala ngati mchenga wa kunyanja,+ otsala ochepa okha pakati pawo ndi amene adzabwerere.+ Chiwonongeko+ chimene Mulungu wakonzera anthu awa chidzabwera mwachilungamo ngati madzi osefukira,+