Yesaya 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 M’tsiku limenelo, padzakhala mizinda isanu m’dziko la Iguputo+ yolankhula chinenero cha ku Kanani+ ndiponso yolumbira+ kwa Yehova wa makamu. Mzinda umodzi udzatchedwa Mzinda wa Chiwonongeko. Aefeso 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+
18 M’tsiku limenelo, padzakhala mizinda isanu m’dziko la Iguputo+ yolankhula chinenero cha ku Kanani+ ndiponso yolumbira+ kwa Yehova wa makamu. Mzinda umodzi udzatchedwa Mzinda wa Chiwonongeko.
25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+