2 Mafumu 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Rabisake akadali chiimire, anapitiriza kulankhula mokweza m’chilankhulo cha Ayuda,+ ndipo anati: “Imvani mawu a mfumu yaikulu,+ mfumu ya Asuri.
28 Choncho Rabisake akadali chiimire, anapitiriza kulankhula mokweza m’chilankhulo cha Ayuda,+ ndipo anati: “Imvani mawu a mfumu yaikulu,+ mfumu ya Asuri.