2 Mbiri 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo+ anapitiriza kulankhula mokuwa+ m’chilankhulo cha Ayuda,+ kwa anthu a ku Yerusalemu amene anali pamwamba pa mpanda, kuti awachititse mantha+ ndi kuwasokoneza n’cholinga choti alande mzindawo. Yesaya 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Rabisake akadali chiimire,+ anapitiriza kulankhula mokweza m’chilankhulo cha Ayuda,+ kuti: “Imvani mawu a mfumu yaikulu, mfumu ya Asuri.+
18 Iwo+ anapitiriza kulankhula mokuwa+ m’chilankhulo cha Ayuda,+ kwa anthu a ku Yerusalemu amene anali pamwamba pa mpanda, kuti awachititse mantha+ ndi kuwasokoneza n’cholinga choti alande mzindawo.
13 Choncho Rabisake akadali chiimire,+ anapitiriza kulankhula mokweza m’chilankhulo cha Ayuda,+ kuti: “Imvani mawu a mfumu yaikulu, mfumu ya Asuri.+