2 Mbiri 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo+ anapitiriza kulankhula mokuwa+ m’chilankhulo cha Ayuda,+ kwa anthu a ku Yerusalemu amene anali pamwamba pa mpanda, kuti awachititse mantha+ ndi kuwasokoneza n’cholinga choti alande mzindawo.
18 Iwo+ anapitiriza kulankhula mokuwa+ m’chilankhulo cha Ayuda,+ kwa anthu a ku Yerusalemu amene anali pamwamba pa mpanda, kuti awachititse mantha+ ndi kuwasokoneza n’cholinga choti alande mzindawo.