2 Mafumu 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Rabisake akadali chiimire, anapitiriza kulankhula mokweza m’chilankhulo cha Ayuda,+ ndipo anati: “Imvani mawu a mfumu yaikulu,+ mfumu ya Asuri. Yesaya 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Rabisake akadali chiimire,+ anapitiriza kulankhula mokweza m’chilankhulo cha Ayuda,+ kuti: “Imvani mawu a mfumu yaikulu, mfumu ya Asuri.+
28 Choncho Rabisake akadali chiimire, anapitiriza kulankhula mokweza m’chilankhulo cha Ayuda,+ ndipo anati: “Imvani mawu a mfumu yaikulu,+ mfumu ya Asuri.
13 Choncho Rabisake akadali chiimire,+ anapitiriza kulankhula mokweza m’chilankhulo cha Ayuda,+ kuti: “Imvani mawu a mfumu yaikulu, mfumu ya Asuri.+