Genesis 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’kupita kwa nthawi Ada anabereka Yabala, amene anakhala tate wa anthu okhala m’mahema+ ndi oweta ziweto.+ Aheberi 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mwa chikhulupiriro, anakhala monga mlendo m’dziko la lonjezo ngati kuti akukhala m’dziko lachilendo.+ Ndipo anali kukhala m’mahema+ pamodzi ndi Isaki+ ndi Yakobo,+ anzake olandira nawo limodzi lonjezolo.+
20 M’kupita kwa nthawi Ada anabereka Yabala, amene anakhala tate wa anthu okhala m’mahema+ ndi oweta ziweto.+
9 Mwa chikhulupiriro, anakhala monga mlendo m’dziko la lonjezo ngati kuti akukhala m’dziko lachilendo.+ Ndipo anali kukhala m’mahema+ pamodzi ndi Isaki+ ndi Yakobo,+ anzake olandira nawo limodzi lonjezolo.+