Genesis 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anyamatawa anakula, ndipo Esau anakhala munthu wodziwa kusaka,+ munthu wokonda kuyenda m’tchire. Koma Yakobo anali kukhala nthawi yambiri m’mahema.+ Iye anali munthu wosalakwa.+ Aheberi 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mwa chikhulupiriro, anakhala monga mlendo m’dziko la lonjezo ngati kuti akukhala m’dziko lachilendo.+ Ndipo anali kukhala m’mahema+ pamodzi ndi Isaki+ ndi Yakobo,+ anzake olandira nawo limodzi lonjezolo.+
27 Anyamatawa anakula, ndipo Esau anakhala munthu wodziwa kusaka,+ munthu wokonda kuyenda m’tchire. Koma Yakobo anali kukhala nthawi yambiri m’mahema.+ Iye anali munthu wosalakwa.+
9 Mwa chikhulupiriro, anakhala monga mlendo m’dziko la lonjezo ngati kuti akukhala m’dziko lachilendo.+ Ndipo anali kukhala m’mahema+ pamodzi ndi Isaki+ ndi Yakobo,+ anzake olandira nawo limodzi lonjezolo.+