-
Salimo 136:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Iye amene anatikumbukira pamene adani anatinyazitsa:+
Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
-