2 Mbiri 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yosiya anagwetsamo maguwa ansembe+ ndi mizati yopatulika.+ Zifaniziro zogoba+ anaziphwanya n’kuziperapera,+ ndipo anagumula zofukizira zonse+ m’dziko lonse la Isiraeli. Atatero anabwerera ku Yerusalemu. Hoseya 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mtima wawo wakhala wachinyengo.+ Tsopano iwo adzapezeka ndi mlandu. “Pali wina amene adzathyola maguwa awo ansembe ndipo adzasakaza zipilala zawo zopatulika.+ Mika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Samariya ndidzamusandutsa bwinja+ ndi malo oyenera kubzalapo mpesa. Miyala yake ndidzaiponya m’chigwa ndipo maziko ake ndidzawafukula n’kuwasiya pamtunda.+
7 Yosiya anagwetsamo maguwa ansembe+ ndi mizati yopatulika.+ Zifaniziro zogoba+ anaziphwanya n’kuziperapera,+ ndipo anagumula zofukizira zonse+ m’dziko lonse la Isiraeli. Atatero anabwerera ku Yerusalemu.
2 Mtima wawo wakhala wachinyengo.+ Tsopano iwo adzapezeka ndi mlandu. “Pali wina amene adzathyola maguwa awo ansembe ndipo adzasakaza zipilala zawo zopatulika.+
6 Samariya ndidzamusandutsa bwinja+ ndi malo oyenera kubzalapo mpesa. Miyala yake ndidzaiponya m’chigwa ndipo maziko ake ndidzawafukula n’kuwasiya pamtunda.+