Ekisodo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye ananenanso kuti: “Ndine Mulungu wa atate ako, Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo.”+ Pamenepo Mose anaphimba nkhope yake, chifukwa anaopa kuyang’ana Mulungu woona. Oweruza 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Manowa anauza mkazi wake kuti: “Ife tifa basi,+ chifukwa taona Mulungu.”+ Mateyu 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ophunzirawo atamva zimenezi, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi ndipo anachita mantha kwambiri.+
6 Iye ananenanso kuti: “Ndine Mulungu wa atate ako, Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo.”+ Pamenepo Mose anaphimba nkhope yake, chifukwa anaopa kuyang’ana Mulungu woona.
6 Ophunzirawo atamva zimenezi, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi ndipo anachita mantha kwambiri.+