Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 26:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Usiku umenewo, Yehova anaonekera kwa iye ndipo anamuuza kuti: “Ine ndine Mulungu wa Abulahamu bambo ako.+ Usaope,+ chifukwa ndili nawe. Ndidzakudalitsa ndi kuchulukitsa mbewu yako chifukwa cha Abulahamu mtumiki wanga.”+

  • Genesis 32:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Atatero, Yakobo anati: “Mulungu wa kholo langa Abulahamu, Mulungu wa bambo anga Isaki,+ inu Yehova munandiuza kuti, ‘Bwerera kudziko lakwanu, kwa abale ako, ndipo ndidzakusamalira.’+

  • Mateyu 22:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 ‘Ine ndine Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo’?+ Iye ndi Mulungu wa anthu amoyo, osati akufa.”+

  • Machitidwe 7:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 ‘Ine ndine Mulungu wa makolo ako. Ndine Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo.’+ Ponjenjemera ndi mantha, Mose sanathenso kupitiriza kuyang’anitsitsa chitsambacho.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena