Genesis 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Potsirizira pake Yehova anauza Yakobo kuti: “Tsopano bwerera kudziko la makolo ako ndi kwa abale ako,+ ndipo ine ndidzakhalabe nawe.”+ Genesis 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndine Mulungu woona wa ku Beteli+ uja, kumene unadzoza mwala+ kuja, kumenenso unachita lonjezo kwa ine.+ Tsopano nyamuka, uchoke kudziko lino, ubwerere kudziko limene unabadwira.’”+
3 Potsirizira pake Yehova anauza Yakobo kuti: “Tsopano bwerera kudziko la makolo ako ndi kwa abale ako,+ ndipo ine ndidzakhalabe nawe.”+
13 Ndine Mulungu woona wa ku Beteli+ uja, kumene unadzoza mwala+ kuja, kumenenso unachita lonjezo kwa ine.+ Tsopano nyamuka, uchoke kudziko lino, ubwerere kudziko limene unabadwira.’”+