Genesis 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Yakobo anakhalabe mādziko la Kanani,+ kumene bambo ake anakhalako ngati mlendo.+