Genesis 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ine ndinadzakhala kwanu kuno ngati mlendo.+ Choncho ndigawireniko malo kuti ndikhale ndi manda angaanga, ndiikemo mkazi wanga.”*+ Genesis 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakupatsa iwe ndi mbewu zako+ madalitso amene analonjeza Abulahamu,+ kuti udzakhale mwini dziko limene ukukhalamo ngati mlendo,+ limene Mulungu anapatsa Abulahamu.”+ Aheberi 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mwa chikhulupiriro, anakhala monga mlendo m’dziko la lonjezo ngati kuti akukhala m’dziko lachilendo.+ Ndipo anali kukhala m’mahema+ pamodzi ndi Isaki+ ndi Yakobo,+ anzake olandira nawo limodzi lonjezolo.+
4 “Ine ndinadzakhala kwanu kuno ngati mlendo.+ Choncho ndigawireniko malo kuti ndikhale ndi manda angaanga, ndiikemo mkazi wanga.”*+
4 Adzakupatsa iwe ndi mbewu zako+ madalitso amene analonjeza Abulahamu,+ kuti udzakhale mwini dziko limene ukukhalamo ngati mlendo,+ limene Mulungu anapatsa Abulahamu.”+
9 Mwa chikhulupiriro, anakhala monga mlendo m’dziko la lonjezo ngati kuti akukhala m’dziko lachilendo.+ Ndipo anali kukhala m’mahema+ pamodzi ndi Isaki+ ndi Yakobo,+ anzake olandira nawo limodzi lonjezolo.+