Yeremiya 48:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amowabuwo adzachita manyazi ndi Kemosi, ngati mmene anthu a mʼnyumba ya Isiraeli achitira manyazi ndi Beteli, mzinda umene ankaudalira.+
13 Amowabuwo adzachita manyazi ndi Kemosi, ngati mmene anthu a mʼnyumba ya Isiraeli achitira manyazi ndi Beteli, mzinda umene ankaudalira.+