Yeremiya 48:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amowabuwo adzachita manyazi ndi Kemosi,+ monga mmene anthu a m’nyumba ya Isiraeli achitira manyazi ndi Beteli, mzinda umene anali kuudalira.+
13 Amowabuwo adzachita manyazi ndi Kemosi,+ monga mmene anthu a m’nyumba ya Isiraeli achitira manyazi ndi Beteli, mzinda umene anali kuudalira.+