1 Mafumu 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno chifaniziro cha ng’ombe chimodzi anakachiika ku Beteli,+ china anakachiika ku Dani.+ Hoseya 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu anthu a ku Beteli, wina adzakuchitaninso zimenezi chifukwa ndinu anthu oipitsitsa.+ Ndithu, mfumu ya Isiraeli adzaikhalitsa chete m’bandakucha.”+ Amosi 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli+ ndipo musabwere ku Giligala.+ Musadutse malire kupita ku Beere-seba+ chifukwa ndithu Giligala adzagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo+ ndipo Beteli adzakhala malo ochitikira zinthu zamatsenga.+
15 Inu anthu a ku Beteli, wina adzakuchitaninso zimenezi chifukwa ndinu anthu oipitsitsa.+ Ndithu, mfumu ya Isiraeli adzaikhalitsa chete m’bandakucha.”+
5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli+ ndipo musabwere ku Giligala.+ Musadutse malire kupita ku Beere-seba+ chifukwa ndithu Giligala adzagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo+ ndipo Beteli adzakhala malo ochitikira zinthu zamatsenga.+