2 Mafumu 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamapeto pa zaka zitatu, Asuriwo analanda mzindawo.+ Anaulanda m’chaka cha 6 cha Hezekiya, kutanthauza chaka cha 9 cha Hoshiya mfumu ya Isiraeli. Chotero Samariya analandidwa.+
10 Pamapeto pa zaka zitatu, Asuriwo analanda mzindawo.+ Anaulanda m’chaka cha 6 cha Hezekiya, kutanthauza chaka cha 9 cha Hoshiya mfumu ya Isiraeli. Chotero Samariya analandidwa.+