Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hoseya 13:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Samariya adzaimbidwa mlandu+ chifukwa iye akupandukira Mulungu wake.+ Iwo adzagwetsedwa ndi lupanga.+ Ana awo adzaphwanyidwaphwanyidwa+ ndipo akazi awo amene ali ndi pakati adzatumbulidwa.”+

  • Amosi 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pali mdani amene wazungulira dziko lonse+ ndipo ameneyo adzakukhalitsa wopanda mphamvu ndipo adzafunkha nsanja zako zokhalamo.’+

  • Mika 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Samariya ndidzamusandutsa bwinja+ ndi malo oyenera kubzalapo mpesa. Miyala yake ndidzaiponya m’chigwa ndipo maziko ake ndidzawafukula n’kuwasiya pamtunda.+

  • Mika 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Anthu inu mukutsatira zochita za Omuri.+ Zochita zonse za anthu a nyumba ya Ahabu, inunso mukuzichita+ ndipo mukuyendera maganizo awo.+ Pa chifukwa chimenechi ndidzakusandutsani chinthu chodabwitsa ndipo anthu a mumzindawo adzakhala oyenera kuwaimbira mluzu.+ Inuyo mudzatonzedwa ndi mitundu ina ya anthu.”+

  • Mika 7:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Dzikoli lidzakhala bwinja chifukwa cha zochita za anthu okhala mmenemo ndi zotsatirapo za zochita zawozo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena