Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 15:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pakuti kupanduka+ n’chimodzimodzi ndi tchimo la kuwombeza,+ ndipo kuchita zinthu modzikuza n’chimodzimodzi ndi kugwiritsa ntchito mphamvu zamatsenga ndiponso aterafi.+ Popeza iwe wakana mawu a Yehova,+ iyenso wakukana kuti usakhalenso mfumu.”+

  • Salimo 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mulungu adzawapeza ndi mlandu.+

      Adzagwa ndi ziwembu zawo zomwe.+

      Muwamwaze chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zawo,+

      Chifukwa iwo akupandukirani.+

  • Ezekieli 20:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “‘“Koma anawo anayamba kundipandukira.+ Sanayende motsatira malamulo anga ndipo sanasunge ndi kutsatira zigamulo zanga, zimene ngati munthu atazitsatira angakhale ndi moyo.+ Iwo anadetsa sabata langa,+ choncho ndinatsimikiza mtima kuwatsanulira mkwiyo wanga, kuti ukali wanga uthere pa iwo m’chipululu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena