Numeri 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano Aisiraeli anali kukhala ku Sitimu.+ Ali kumeneko, iwo anayamba kuchita chiwerewere ndi akazi a ku Mowabu.+ Deuteronomo 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova atakutumani kuchokera ku Kadesi-barinea+ kuti, ‘Kwerani ndi kukatenga dziko limene ndidzakupatsani kuti likhale lanu,’ pamenepo munapandukiranso malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ ndipo simunasonyeze chikhulupiriro+ mwa iye komanso simunamvere mawu ake.+ 1 Mafumu 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno anayamba kuuza munthu wa Mulungu woona yemwe anachokera ku Yuda uja, kuti: “Nazi zimene Yehova wanena, ‘Chifukwa chakuti wapandukira+ lamulo la Yehova, ndipo sunasunge lamulo limene Yehova Mulungu wako anakulamula,+
25 Tsopano Aisiraeli anali kukhala ku Sitimu.+ Ali kumeneko, iwo anayamba kuchita chiwerewere ndi akazi a ku Mowabu.+
23 Yehova atakutumani kuchokera ku Kadesi-barinea+ kuti, ‘Kwerani ndi kukatenga dziko limene ndidzakupatsani kuti likhale lanu,’ pamenepo munapandukiranso malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ ndipo simunasonyeze chikhulupiriro+ mwa iye komanso simunamvere mawu ake.+
21 Ndiyeno anayamba kuuza munthu wa Mulungu woona yemwe anachokera ku Yuda uja, kuti: “Nazi zimene Yehova wanena, ‘Chifukwa chakuti wapandukira+ lamulo la Yehova, ndipo sunasunge lamulo limene Yehova Mulungu wako anakulamula,+