Numeri 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Aroni aikidwe m’manda, agone ndi makolo ake,+ pakuti sadzalowa m’dziko limene ndidzapatse ana a Isiraeli. Izi zili choncho chifukwa amuna inu munapandukira malangizo anga okhudza madzi a ku Meriba.+ Numeri 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndiyeno mngelo wa Yehova uja anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani wakhala ukukwapula bulu wako maulendo atatu onsewa? Inetu ndabwera kudzakutchingira njira, chifukwa uli pa ulendo wothamangira kukachita zotsutsana ndi chifuniro changa.+
24 “Aroni aikidwe m’manda, agone ndi makolo ake,+ pakuti sadzalowa m’dziko limene ndidzapatse ana a Isiraeli. Izi zili choncho chifukwa amuna inu munapandukira malangizo anga okhudza madzi a ku Meriba.+
32 Ndiyeno mngelo wa Yehova uja anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani wakhala ukukwapula bulu wako maulendo atatu onsewa? Inetu ndabwera kudzakutchingira njira, chifukwa uli pa ulendo wothamangira kukachita zotsutsana ndi chifuniro changa.+