Deuteronomo 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngakhale kuti munamva mawu amenewa, simunakhulupirire Yehova Mulungu wanu,+ Salimo 106:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo anayamba kunyansidwa ndi dziko losiririka,+Ndipo analibe chikhulupiriro m’mawu ake.+ Aheberi 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho, tikuona kuti sakanatha kulowa mu mpumulowo chifukwa anali opanda chikhulupiriro.+