Salimo 78:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti iwo sanakhulupirire Mulungu.+Sanakhulupirire kuti iye adzawapulumutsa.+ Salimo 106:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo anayamba kunyansidwa ndi dziko losiririka,+Ndipo analibe chikhulupiriro m’mawu ake.+ Aheberi 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi paja ndi ndani amene anamva koma n’kupsetsa mtima Mulungu?+ Kodi si anthu onse amene anatuluka m’dziko la Iguputo motsogoleredwa ndi Mose?+ Aheberi 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho, tikuona kuti sakanatha kulowa mu mpumulowo chifukwa anali opanda chikhulupiriro.+ Yuda 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zinthu zonse, ndikufuna kukukumbutsani kuti,+ ngakhale kuti Yehova anapulumutsa anthu ake powatulutsa m’dziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+
16 Kodi paja ndi ndani amene anamva koma n’kupsetsa mtima Mulungu?+ Kodi si anthu onse amene anatuluka m’dziko la Iguputo motsogoleredwa ndi Mose?+
5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zinthu zonse, ndikufuna kukukumbutsani kuti,+ ngakhale kuti Yehova anapulumutsa anthu ake powatulutsa m’dziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+