Aroma 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa+ kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatipatsa chiyembekezo+ chifukwa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa.+ 2 Petulo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Okondedwa, iyi tsopano ndi kalata yachiwiri imene ndikukulemberani, ndipo monga yoyamba ija,+ ndikulimbikitsa mphamvu zanu zotha kuganiza bwino mwa kukukumbutsani,+
4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa+ kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatipatsa chiyembekezo+ chifukwa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa.+
3 Okondedwa, iyi tsopano ndi kalata yachiwiri imene ndikukulemberani, ndipo monga yoyamba ija,+ ndikulimbikitsa mphamvu zanu zotha kuganiza bwino mwa kukukumbutsani,+