Ekisodo 12:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Zaka 430 zimenezi zitatha, pa tsiku lomwe zinatha, makamu onse a Yehova anatuluka m’dziko la Iguputo.+ Deuteronomo 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma asadzichulukitsire mahatchi+ kapena kuchititsa anthu kubwerera ku Iguputo kuti akakhale ndi mahatchi ochuluka+ pakuti Yehova wakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’
41 Zaka 430 zimenezi zitatha, pa tsiku lomwe zinatha, makamu onse a Yehova anatuluka m’dziko la Iguputo.+
16 Koma asadzichulukitsire mahatchi+ kapena kuchititsa anthu kubwerera ku Iguputo kuti akakhale ndi mahatchi ochuluka+ pakuti Yehova wakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’