Numeri 14:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “‘“Ine Yehova ndalankhula, mudzandifunse ngati sindidzawafafaniza m’chipululu mommuno anthu oipa onsewa,+ amene agwirizana kuti atsutsane ndi ine. Onse adzathera m’chipululu mommuno.+ 1 Akorinto 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale zinali choncho, ambiri a iwo Mulungu sanakondwere+ nawo, ndipo anathana+ nawo m’chipululu. Aheberi 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho, tikuona kuti sakanatha kulowa mu mpumulowo chifukwa anali opanda chikhulupiriro.+
35 “‘“Ine Yehova ndalankhula, mudzandifunse ngati sindidzawafafaniza m’chipululu mommuno anthu oipa onsewa,+ amene agwirizana kuti atsutsane ndi ine. Onse adzathera m’chipululu mommuno.+
5 Ngakhale zinali choncho, ambiri a iwo Mulungu sanakondwere+ nawo, ndipo anathana+ nawo m’chipululu.