Numeri 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Chifukwa Yehova analephera kufikitsa anthuwo kudziko limene anawalumbirira, anangowaphera m’chipululu.’+ Ezekieli 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ine ndinakweza dzanja langa powalumbirira m’chipululu+ kuti sindidzawalowetsa m’dziko limene ndinawapatsa, dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ (dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse)+ Yuda 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zinthu zonse, ndikufuna kukukumbutsani kuti,+ ngakhale kuti Yehova anapulumutsa anthu ake powatulutsa m’dziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+
16 ‘Chifukwa Yehova analephera kufikitsa anthuwo kudziko limene anawalumbirira, anangowaphera m’chipululu.’+
15 Ine ndinakweza dzanja langa powalumbirira m’chipululu+ kuti sindidzawalowetsa m’dziko limene ndinawapatsa, dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ (dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse)+
5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zinthu zonse, ndikufuna kukukumbutsani kuti,+ ngakhale kuti Yehova anapulumutsa anthu ake powatulutsa m’dziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+