Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 44:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mwatisandutsa chitonzo kwa anthu oyandikana nafe,+

      Mwatisandutsa chinthu chonyozeka ndi choseketsa kwa onse otizungulira.+

  • Yeremiya 51:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 “Tamva mawu otonza+ ndipo tachita manyazi.+ Manyazi atiphimba nkhope+ chifukwa alendo aukira malo oyera m’nyumba ya Yehova.”+

  • Maliro 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Inu Yehova, kumbukirani zimene zatichitikira.+ Tiyang’aneni kuti muone chitonzo chathu.+

  • Danieli 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Inu Yehova, nthawi zonse mumachita zinthu zolungama.+ Chonde, chotsani mkwiyo wanu waukulu pa Yerusalemu, phiri lanu loyera.+ Pakuti chifukwa cha machimo athu ndi zolakwa za makolo athu,+ Yerusalemu ndi anthu anu takhala chinthu chotonzedwa ndi anthu onse otizungulira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena