Oweruza 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kodi aliyense amene mulungu wako Kemosi+ wakuchititsa kuti umugonjetse, si amene udzam’gonjetsa? Chotero aliyense amene Yehova Mulungu wathu wam’gonjetsa pamaso pathu ndi amenenso ife tidzam’gonjetsa.+ 1 Mafumu 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anamangira Kemosi+ malo okwezeka,+ chinthu chonyansa+ cha Mowabu, paphiri+ lomwe linali patsogolo+ pa Yerusalemu. Anamangiranso Moleki malo okwezeka, yemwe ndi chinthu chonyansa cha ana a Amoni. Yesaya 45:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthu adzachita manyazi ndipo onsewo adzanyozeka. Anthu opanga mafano adzayenda monyozeka onse pamodzi.+
24 Kodi aliyense amene mulungu wako Kemosi+ wakuchititsa kuti umugonjetse, si amene udzam’gonjetsa? Chotero aliyense amene Yehova Mulungu wathu wam’gonjetsa pamaso pathu ndi amenenso ife tidzam’gonjetsa.+
7 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anamangira Kemosi+ malo okwezeka,+ chinthu chonyansa+ cha Mowabu, paphiri+ lomwe linali patsogolo+ pa Yerusalemu. Anamangiranso Moleki malo okwezeka, yemwe ndi chinthu chonyansa cha ana a Amoni.
16 Anthu adzachita manyazi ndipo onsewo adzanyozeka. Anthu opanga mafano adzayenda monyozeka onse pamodzi.+