7 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anamangira Kemosi+ malo okwezeka,+ chinthu chonyansa+ cha Mowabu, paphiri+ lomwe linali patsogolo+ pa Yerusalemu. Anamangiranso Moleki malo okwezeka, yemwe ndi chinthu chonyansa cha ana a Amoni.
7 Inu mudzagwidwa ndi adani chifukwa mukudalira ntchito zanu ndi chuma chanu.+ Kemosi+ adzatengedwa kupita ku ukapolo+ pamodzi ndi ansembe ake ndi akalonga ake.+