Numeri 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsoka iwe Mowabu! Mudzawonongedwa, inu anthu a Kemosi!+ Iye adzapangitsa ana ake aamuna kukhala othawa kwawo, ndipo adzasandutsa ana ake aakazi kukhala akapolo a Sihoni, mfumu ya Aamori.
29 Tsoka iwe Mowabu! Mudzawonongedwa, inu anthu a Kemosi!+ Iye adzapangitsa ana ake aamuna kukhala othawa kwawo, ndipo adzasandutsa ana ake aakazi kukhala akapolo a Sihoni, mfumu ya Aamori.