4 Mkaziyo anavala zovala zofiirira+ ndi zofiira kwambiri.+ Anadzikongoletsa ndi golide, ndi mwala winawake wamtengo wapatali, ndiponso ngale.+ M’dzanja lake, anali ndi kapu yagolide+ yodzaza ndi zonyansa+ ndi zinthu zodetsedwa zokhudzana ndi dama lake.+