Ekisodo 34:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Musadzipangire milungu ya mafano opangidwa ndi chitsulo chosungunula.+ Levitiko 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musatembenukire kwa milungu yopanda pake,+ ndipo musadzipangire milungu yachitsulo chosungunula.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Numeri 33:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Mukapitikitse anthu onse a m’dzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala,+ ndi mafano awo onse achitsulo.+ Mukawonongenso malo awo onse opatulika olambirira.+
4 Musatembenukire kwa milungu yopanda pake,+ ndipo musadzipangire milungu yachitsulo chosungunula.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
52 Mukapitikitse anthu onse a m’dzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala,+ ndi mafano awo onse achitsulo.+ Mukawonongenso malo awo onse opatulika olambirira.+