Ekisodo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+ Deuteronomo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Musamale kuti musachite zinthu zokuwonongetsani,+ kutinso musadzipangire chifaniziro, chifaniziro cha chinthu chilichonse, chachimuna kapena chachikazi,+ Yesaya 44:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu onse opanga zifaniziro zosema ndi opanda pake,+ ndipo mafano awo okondedwa adzakhala opanda phindu.+ Monga mboni zawo, mafanowo saona chilichonse ndipo sadziwa chilichonse,+ kuti anthu opanga mafanowo achite manyazi.+
4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+
16 Musamale kuti musachite zinthu zokuwonongetsani,+ kutinso musadzipangire chifaniziro, chifaniziro cha chinthu chilichonse, chachimuna kapena chachikazi,+
9 Anthu onse opanga zifaniziro zosema ndi opanda pake,+ ndipo mafano awo okondedwa adzakhala opanda phindu.+ Monga mboni zawo, mafanowo saona chilichonse ndipo sadziwa chilichonse,+ kuti anthu opanga mafanowo achite manyazi.+