Salimo 47:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti Yehova, Wam’mwambamwamba, ndi wochititsa mantha,+Ndiye Mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.+ Salimo 66:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Bwerani anthu inu, kuti muone ntchito za Mulungu.+Zimene wachitira ana a anthu ndi zochititsa mantha.+ Salimo 68:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mulungu akamatuluka m’malo ake opatulika aulemerero, amachititsa mantha.+Iye ndi Mulungu wa Isiraeli, wopereka mphamvu ndi nyonga kwa anthu.+Mulungu adalitsike.+
2 Pakuti Yehova, Wam’mwambamwamba, ndi wochititsa mantha,+Ndiye Mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.+
5 Bwerani anthu inu, kuti muone ntchito za Mulungu.+Zimene wachitira ana a anthu ndi zochititsa mantha.+
35 Mulungu akamatuluka m’malo ake opatulika aulemerero, amachititsa mantha.+Iye ndi Mulungu wa Isiraeli, wopereka mphamvu ndi nyonga kwa anthu.+Mulungu adalitsike.+