Salimo 66:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muuzeni Mulungu kuti: “Ntchito zanu ndi zochititsadi mantha!+Chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zanu, adani anu adzabwera kwa inu mogonjera.+ Zefaniya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzawachititsa mantha,+ pakuti adzawondetsa milungu yonse ya padziko lapansi.+ Pamenepo anthu adzamugwadira,+ aliyense pamalo pake, zilumba zonse za mitundu ya anthu zidzamugwadira.+
3 Muuzeni Mulungu kuti: “Ntchito zanu ndi zochititsadi mantha!+Chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zanu, adani anu adzabwera kwa inu mogonjera.+
11 Yehova adzawachititsa mantha,+ pakuti adzawondetsa milungu yonse ya padziko lapansi.+ Pamenepo anthu adzamugwadira,+ aliyense pamalo pake, zilumba zonse za mitundu ya anthu zidzamugwadira.+