Yesaya 42:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye sadzatsala pang’ono kuzima kapena kuphwanyidwa mpaka atakhazikitsa chilungamo padziko lapansi.+ Zilumba zidzadikirira lamulo lake.+ Yesaya 49:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndimvereni zilumba inu,+ ndipo mvetserani, inu mitundu ya anthu akutali.+ Yehova anandiitana+ ndili m’mimba.+ Ndili mkati mwa mayi anga, anatchula dzina langa.+
4 Iye sadzatsala pang’ono kuzima kapena kuphwanyidwa mpaka atakhazikitsa chilungamo padziko lapansi.+ Zilumba zidzadikirira lamulo lake.+
49 Ndimvereni zilumba inu,+ ndipo mvetserani, inu mitundu ya anthu akutali.+ Yehova anandiitana+ ndili m’mimba.+ Ndili mkati mwa mayi anga, anatchula dzina langa.+