Salimo 71:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuyambira ndili m’mimba mwa mayi anga inu mwandithandiza.+Inu ndi amene munanditulutsa m’mimba mwa mayi anga.+Ndimatamanda inu nthawi zonse.+ Yesaya 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova, amene anakupanga+ ndiponso amene anakuumba,+ amene anali kukuthandiza ngakhale pamene unali m’mimba,+ wanena kuti, ‘Usachite mantha,+ iwe mtumiki wanga Yakobo, ndiponso iwe Yesuruni,+ amene ndakusankha. Yesaya 46:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Inu a nyumba ya Yakobo ndimvetsereni. Ndimvetsereni inu nonse otsala a m’nyumba ya Isiraeli,+ inu amene ndinakunyamulani kuyambira pamene munabadwa, ndiponso inu amene ndinakusamalirani kuyambira pamene munatuluka m’mimba.+
6 Kuyambira ndili m’mimba mwa mayi anga inu mwandithandiza.+Inu ndi amene munanditulutsa m’mimba mwa mayi anga.+Ndimatamanda inu nthawi zonse.+
2 Yehova, amene anakupanga+ ndiponso amene anakuumba,+ amene anali kukuthandiza ngakhale pamene unali m’mimba,+ wanena kuti, ‘Usachite mantha,+ iwe mtumiki wanga Yakobo, ndiponso iwe Yesuruni,+ amene ndakusankha.
3 “Inu a nyumba ya Yakobo ndimvetsereni. Ndimvetsereni inu nonse otsala a m’nyumba ya Isiraeli,+ inu amene ndinakunyamulani kuyambira pamene munabadwa, ndiponso inu amene ndinakusamalirani kuyambira pamene munatuluka m’mimba.+