Salimo 34:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndidzatamanda Yehova nthawi zonse.+Ndidzamutamanda ndi pakamwa panga mosalekeza.+