Hoseya 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Sindidzamulola kutchulanso mayina a zifaniziro za Baala,+ ndipo iye sadzakumbukiranso mayina awo.+ Zekariya 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wa makamu wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzathetsa mayina a mafano m’dziko lonseli+ ndipo mafanowo sadzakumbukiridwanso. M’dzikoli ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.+
17 “‘Sindidzamulola kutchulanso mayina a zifaniziro za Baala,+ ndipo iye sadzakumbukiranso mayina awo.+
2 Yehova wa makamu wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzathetsa mayina a mafano m’dziko lonseli+ ndipo mafanowo sadzakumbukiridwanso. M’dzikoli ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.+